Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 6:15, 16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mtumiki wa munthu wa Mulungu woona atadzuka mʼmawa nʼkutuluka panja, anaona kuti gulu lankhondo lazungulira mzindawo ndi mahatchi ndi magaleta ankhondo. Nthawi yomweyo mtumikiyo anauza mbuye wake kuti: “Mayo ine mbuyanga! Titani?” 16 Koma iye anati: “Usaope,+ ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi iwowo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena