Yeremiya 37:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Akalongawo anakwiyira kwambiri Yeremiya+ ndipo anamumenya nʼkumutsekera*+ mʼnyumba ya Yehonatani mlembi, imene anaisandutsa ndende.
15 Akalongawo anakwiyira kwambiri Yeremiya+ ndipo anamumenya nʼkumutsekera*+ mʼnyumba ya Yehonatani mlembi, imene anaisandutsa ndende.