Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 24:20, 21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Mothandizidwa ndi mzimu wa Mulungu, Zekariya mwana wa wansembe Yehoyada+ anaimirira pamalo okwera nʼkuyamba kuuza anthuwo kuti: “Mulungu woona wanena kuti, ‘Nʼchifukwa chiyani mukuphwanya malamulo a Yehova? Zinthutu sizikukuyenderani bwino. Poti mwamusiya Yehova, iyenso akusiyani.’”+ 21 Koma anthuwo anamʼkonzera chiwembu+ ndipo anamʼponya miyala pabwalo la nyumba ya Yehova, atalamulidwa ndi mfumu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena