Genesis 27:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Atamva mawu a bambo akewa, Esau anayamba kulira ndi kukuwa mogonthetsa mʼkhutu, komanso mowawidwa mtima kwambiri. Iye anachonderera bambo ake kuti: “Bambo ndidalitseni, ndidalitseni inenso chonde!”+
34 Atamva mawu a bambo akewa, Esau anayamba kulira ndi kukuwa mogonthetsa mʼkhutu, komanso mowawidwa mtima kwambiri. Iye anachonderera bambo ake kuti: “Bambo ndidalitseni, ndidalitseni inenso chonde!”+