Salimo 118:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova ali kumbali yanga, sindidzaopa.+ Munthu angandichite chiyani?+ Danieli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngati mungatiponyere mungʼanjo yoyaka moto, Mulungu wathu amene tikumutumikira akhoza kutipulumutsa. Iye akhozanso kutipulumutsa mʼmanja mwanu mfumu.+ Luka 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Komanso ndikukuuzani mabwenzi anga,+ musamaope amene amapha thupi lokha, omwe sangathe kuchita zoposa pamenepa.+
17 Ngati mungatiponyere mungʼanjo yoyaka moto, Mulungu wathu amene tikumutumikira akhoza kutipulumutsa. Iye akhozanso kutipulumutsa mʼmanja mwanu mfumu.+
4 Komanso ndikukuuzani mabwenzi anga,+ musamaope amene amapha thupi lokha, omwe sangathe kuchita zoposa pamenepa.+