1 Timoteyo 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akulu amene amatsogolera bwino+ azilemekezedwa kwambiri,+ makamaka amene amachita khama polankhula Mawu a Mulungu ndiponso kuphunzitsa.+ Aheberi 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Muzimvera amene akukutsogolerani+ ndipo muziwagonjera+ chifukwa iwo amayangʼanira miyoyo yanu ndipo adzayankha mlandu.+ Muzichita zimenezi kuti azigwira ntchito yawo mosangalala osati modandaula, chifukwa akatero sizingakuyendereni bwino.
17 Akulu amene amatsogolera bwino+ azilemekezedwa kwambiri,+ makamaka amene amachita khama polankhula Mawu a Mulungu ndiponso kuphunzitsa.+
17 Muzimvera amene akukutsogolerani+ ndipo muziwagonjera+ chifukwa iwo amayangʼanira miyoyo yanu ndipo adzayankha mlandu.+ Muzichita zimenezi kuti azigwira ntchito yawo mosangalala osati modandaula, chifukwa akatero sizingakuyendereni bwino.