Luka 24:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kodi sikunali koyenera kuti Khristu amve zowawa zonsezi+ nʼkulowa mu ulemerero wake?”+ Aheberi 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngakhale kuti anali Mwana wa Mulungu, anaphunzira kumvera chifukwa cha mavuto amene anakumana nawo.+
8 Ngakhale kuti anali Mwana wa Mulungu, anaphunzira kumvera chifukwa cha mavuto amene anakumana nawo.+