Yohane 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye ananyamula yekha mtengo wozunzikirapo* nʼkutuluka kupita kumalo amene ankatchulidwa kuti Chibade,+ koma pa Chiheberi ankatchulidwa kuti Gologota.+
17 Iye ananyamula yekha mtengo wozunzikirapo* nʼkutuluka kupita kumalo amene ankatchulidwa kuti Chibade,+ koma pa Chiheberi ankatchulidwa kuti Gologota.+