Yesaya 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa+ tili ngati zizindikiro+ ndiponso ngati zodabwitsa mu Isiraeli, zochokera kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, amene amakhala mʼphiri la Ziyoni.
18 Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa+ tili ngati zizindikiro+ ndiponso ngati zodabwitsa mu Isiraeli, zochokera kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, amene amakhala mʼphiri la Ziyoni.