Salimo 95:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho ndinalumbira nditakwiya kuti: “Sadzalowa mumpumulo wanga.”+ Aheberi 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho ndinalumbira nditakwiya kuti, ‘Sadzalowa mumpumulo wanga.’”+