Ekisodo 31:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chimenechi nʼchizindikiro pakati pa ine ndi Aisiraeli mpaka kalekale,+ chifukwa mʼmasiku 6, Yehova anapanga kumwamba ndi dziko lapansi, koma pa tsiku la 7 anapuma pa ntchito yake ndipo anasangalala.’”+
17 Chimenechi nʼchizindikiro pakati pa ine ndi Aisiraeli mpaka kalekale,+ chifukwa mʼmasiku 6, Yehova anapanga kumwamba ndi dziko lapansi, koma pa tsiku la 7 anapuma pa ntchito yake ndipo anasangalala.’”+