7 Chifukwa iye ndi Mulungu wathu
Ndipo ife ndi anthu amene iye akuweta,
Nkhosa zimene akuzisamalira.+
Lero anthu inu mukamvera mawu ake,+
8 Musaumitse mitima yanu ngati mmene makolo anu anachitira ku Meriba,+
Ngati mmene anachitira ku Masa mʼchipululu,+