Ekisodo 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Mose ndi Yoswa mtumiki wake ananyamuka,+ ndipo Mose anakwera mʼphiri la Mulungu woona.+ Deuteronomo 1:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Yoswa mwana wa Nuni, amene akukutumikira+ ndi amene akalowe mʼdzikomo.+ Umulimbitse,*+ chifukwa ndi amene adzatsogolere Aisiraeli pokatenga dzikolo kukhala lawo.”)
38 Yoswa mwana wa Nuni, amene akukutumikira+ ndi amene akalowe mʼdzikomo.+ Umulimbitse,*+ chifukwa ndi amene adzatsogolere Aisiraeli pokatenga dzikolo kukhala lawo.”)