Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 23:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Yehova wanena kuti: “Kodi mawu anga safanana ndi moto?+ Kodi safanana ndi hamala imene imaphwanya thanthwe?”+

  • 1 Atesalonika 2:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndithudi, nʼchifukwa chake ifenso timathokoza Mulungu mosalekeza,+ chifukwa pamene munalandira mawu a Mulungu amene munamva kwa ife, simunawalandire monga mawu a anthu, koma mmene alilidi, monga mawu a Mulungu. Mawu amenewa akugwiranso ntchito mwa inu okhulupirira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena