-
Yakobo 1:2-4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Abale anga, muzisangalala kwambiri pamene mukukumana ndi mayesero osiyanasiyana,+ 3 chifukwa monga mukudziwira, chikhulupiriro chanu chikakhalabe cholimba pamene mukuyesedwa, mumaphunzira kukhala opirira.+ 4 Koma lolani kuti kupirirako kumalize kugwira ntchito yake, kuti mukhale okwanira ndi opanda cholakwa pa mbali iliyonse, kapena kuti mukhale ndi makhalidwe onse abwino.+
-