Akolose 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawu a Khristu akhazikike mwa inu ndipo akupatseni nzeru zonse. Pitirizani kuphunzitsana ndi kulimbikitsana* ndi masalimo,+ nyimbo zotamanda Mulungu komanso nyimbo zauzimu zoyamikira. Pitirizani kuimbira Yehova* mʼmitima yanu.+
16 Mawu a Khristu akhazikike mwa inu ndipo akupatseni nzeru zonse. Pitirizani kuphunzitsana ndi kulimbikitsana* ndi masalimo,+ nyimbo zotamanda Mulungu komanso nyimbo zauzimu zoyamikira. Pitirizani kuimbira Yehova* mʼmitima yanu.+