21 Chifukwa chiyani? Kuti mmene uchimo unalamulira ngati mfumu pamodzi ndi imfa,+ nakonso kukoma mtima kwakukulu kulamulire ngati mfumu kudzera mʼchilungamo. Ndipo zimenezi zidzachititsa kuti anthu apeze moyo wosatha kudzera mwa Yesu Khristu Ambuye wathu.+