Miyambo 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mawu akachuluka sipalephera kukhala zolakwika,+Koma amene amalamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+ Miyambo 17:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Munthu wodziwa zinthu amayamba waganiza asanalankhule,+Ndipo munthu wozindikira amapitiriza kukhala wodekha.+
19 Mawu akachuluka sipalephera kukhala zolakwika,+Koma amene amalamulira milomo yake amachita zinthu mwanzeru.+
27 Munthu wodziwa zinthu amayamba waganiza asanalankhule,+Ndipo munthu wozindikira amapitiriza kukhala wodekha.+