-
Tito 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mawu amenewa ndi oona, ndipo ndikufuna kuti upitirize kutsindika zinthu zimenezi, kuti amene akhulupirira Mulungu aziganizira kwambiri mmene angapitirizire kuchita ntchito zabwino. Zimenezi nʼzabwino ndiponso zothandiza kwa anthu.
-