Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 39:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Ine ndinanena kuti: “Ndidzakhala wosamala ndi zochita zanga

      Kuti ndisachimwe ndi lilime langa.+

      Ndidzaphimba pakamwa panga kuti ndisalankhule+

      Nthawi zonse pamene woipa ali pamaso panga.”

  • Mateyu 15:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chimene chimalowa mʼkamwa mwa munthu si chimene chimamuipitsa, koma chimene chimatuluka mʼkamwa mwake nʼchimene chimamuipitsa.”+

  • Mateyu 15:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma chilichonse chimene chimatuluka pakamwa chimachokera mumtima ndipo zinthu zimenezo ndi zimene zimaipitsa munthu.+

  • Maliko 7:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Zoipa zonsezi zimatuluka mumtima mwa munthu ndipo zimamuipitsa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena