Mateyu 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Osangalala ndi anthu amene amabweretsa mtendere+ chifukwa adzatchedwa ana a Mulungu. 1 Petulo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ayenera kusiya kuchita zoipa+ nʼkumachita zabwino.+ Ayeneranso kuyesetsa kumakhala mwamtendere ndi ena komanso kuulimbikitsa.+
11 Ayenera kusiya kuchita zoipa+ nʼkumachita zabwino.+ Ayeneranso kuyesetsa kumakhala mwamtendere ndi ena komanso kuulimbikitsa.+