Yesaya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sambani, dziyeretseni.+Chotsani zochita zanu zoipa pamaso panga.Lekani kuchita zoipa.+