2 Akorinto 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwatu ngakhale kuti mavuto* amene tikukumana nawo ndi akanthawi ndiponso aangʼono, akutichititsa kuti tilandire ulemerero umene ukukulirakulira komanso womwe ndi wamuyaya,+ 2 Timoteyo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mogwirizana ndi Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+
17 Chifukwatu ngakhale kuti mavuto* amene tikukumana nawo ndi akanthawi ndiponso aangʼono, akutichititsa kuti tilandire ulemerero umene ukukulirakulira komanso womwe ndi wamuyaya,+
12 Pajatu onse ofuna kukhala ndi moyo wodzipereka kwa Mulungu mogwirizana ndi Khristu Yesu, nawonso adzazunzidwa.+