-
2 Atesalonika 1:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Koma inu amene mukuvutika mudzapatsidwa mpumulo pamodzi ndi ife pa nthawi imene Ambuye Yesu adzaonekere*+ kuchokera kumwamba limodzi ndi angelo ake amphamvu+ 8 mʼmoto walawilawi. Pa nthawi imeneyo adzabwezera chilango kwa anthu osadziwa Mulungu komanso kwa anthu amene samvera uthenga wabwino wonena za Ambuye wathu Yesu.+
-