2 Akorinto 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Sikuti ndife olamulira chikhulupiriro chanu,+ koma ndife antchito anzanu kuti muzisangalala, popeza ndinu okhazikika chifukwa cha chikhulupiriro chanu.
24 Sikuti ndife olamulira chikhulupiriro chanu,+ koma ndife antchito anzanu kuti muzisangalala, popeza ndinu okhazikika chifukwa cha chikhulupiriro chanu.