2 Akorinto 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwatu ngakhale kuti mavuto* amene tikukumana nawo ndi akanthawi ndiponso aangʼono, akutichititsa kuti tilandire ulemerero umene ukukulirakulira komanso womwe ndi wamuyaya,+ 1 Atesalonika 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tinkachita zimenezi nʼcholinga choti mupitirize kuyenda mʼnjira imene Mulungu amafuna.+ Iye ndi amene akukuitanani kuti mulowe mu Ufumu wake+ ndi kulandira ulemerero.+
17 Chifukwatu ngakhale kuti mavuto* amene tikukumana nawo ndi akanthawi ndiponso aangʼono, akutichititsa kuti tilandire ulemerero umene ukukulirakulira komanso womwe ndi wamuyaya,+
12 Tinkachita zimenezi nʼcholinga choti mupitirize kuyenda mʼnjira imene Mulungu amafuna.+ Iye ndi amene akukuitanani kuti mulowe mu Ufumu wake+ ndi kulandira ulemerero.+