Machitidwe 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atazindikira zimenezi, iye anapita kunyumba kwa Mariya, mayi ake a Yohane wotchedwanso Maliko.+ Kumeneko anthu ambiri anali atasonkhana nʼkumapemphera.
12 Atazindikira zimenezi, iye anapita kunyumba kwa Mariya, mayi ake a Yohane wotchedwanso Maliko.+ Kumeneko anthu ambiri anali atasonkhana nʼkumapemphera.