Aefeso 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mogwirizana ndi iye, nyumba yonse, popeza ndi yolumikizana bwino,+ ikukula nʼkukhala kachisi woyera wa Yehova.*+
21 Mogwirizana ndi iye, nyumba yonse, popeza ndi yolumikizana bwino,+ ikukula nʼkukhala kachisi woyera wa Yehova.*+