Aefeso 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa poyamba munali ngati mdima, koma pano muli ngati kuwala+ popeza ndinu ogwirizana ndi Ambuye.+ Pitirizani kuyenda ngati ana a kuwala. Akolose 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anatipulumutsa ku ulamuliro wa mdima,+ nʼkutisamutsira mu ufumu wa Mwana wake wokondedwa.
8 Chifukwa poyamba munali ngati mdima, koma pano muli ngati kuwala+ popeza ndinu ogwirizana ndi Ambuye.+ Pitirizani kuyenda ngati ana a kuwala.