Agalatiya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Abale, munaitanidwa kuti mukhale aufulu. Koma musagwiritse ntchito ufulu umenewu ngati mwayi woti muzichita zimene thupi lomwe si langwiro limalakalaka.+ Mʼmalomwake muzilola kuti chikondi chizikulimbikitsani kutumikirana.+
13 Abale, munaitanidwa kuti mukhale aufulu. Koma musagwiritse ntchito ufulu umenewu ngati mwayi woti muzichita zimene thupi lomwe si langwiro limalakalaka.+ Mʼmalomwake muzilola kuti chikondi chizikulimbikitsani kutumikirana.+