Levitiko 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Anthu aimvi uziwagwadira,+ munthu wachikulire uzimupatsa ulemu+ ndipo uziopa Mulungu wako.+ Ine ndine Yehova. Aroma 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pokonda abale, muzikhala ndi chikondi chenicheni. Pa nkhani yosonyezana ulemu, muziyamba ndi inuyo.+ Aroma 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muzipereka kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, mʼpatseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, mʼpatseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, mʼpatseni ulemu wake.+
32 Anthu aimvi uziwagwadira,+ munthu wachikulire uzimupatsa ulemu+ ndipo uziopa Mulungu wako.+ Ine ndine Yehova.
10 Pokonda abale, muzikhala ndi chikondi chenicheni. Pa nkhani yosonyezana ulemu, muziyamba ndi inuyo.+
7 Muzipereka kwa onse zimene amafuna. Amene amafuna msonkho, mʼpatseni msonkho.+ Amene amafuna ndalama ya chiphaso, mʼpatseni ndalama ya chiphaso. Amene amafuna kuopedwa, muopeni.+ Amene amafuna kupatsidwa ulemu, mʼpatseni ulemu wake.+