1 Petulo 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma sindikufuna kuti wina wa inu azivutika chifukwa choti wayamba kuba, kupha anthu, kuchita zoipa kapena chifukwa choti akulowerera nkhani za eni.+
15 Koma sindikufuna kuti wina wa inu azivutika chifukwa choti wayamba kuba, kupha anthu, kuchita zoipa kapena chifukwa choti akulowerera nkhani za eni.+