-
Yohane 8:46Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
46 Ndi ndani wa inu amene angapereke umboni wosonyeza kuti ndachita tchimo? Ngati ndimanena zoona, nʼchifukwa chiyani simundikhulupirira?
-