Akolose 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nʼchifukwa chake ifenso, kuyambira tsiku limene tinamva zimenezo, sitinasiye kukupemphererani.+ Takhala tikupempha kuti mudziwe molondola+ chifuniro cha Mulungu ndiponso kuti mukhale ndi nzeru zonse komanso muzimvetsetsa zinthu zauzimu.+
9 Nʼchifukwa chake ifenso, kuyambira tsiku limene tinamva zimenezo, sitinasiye kukupemphererani.+ Takhala tikupempha kuti mudziwe molondola+ chifuniro cha Mulungu ndiponso kuti mukhale ndi nzeru zonse komanso muzimvetsetsa zinthu zauzimu.+