Yohane 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Moyo wosatha adzaupeza+ akamaphunzira ndi kudziwa za inu, Mulungu yekhayo amene ndi woona,+ komanso za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+ Aheberi 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma chakudya chotafuna ndi cha anthu aakulu mwauzimu, amene amatha kusiyanitsa zoyenera ndi zosayenera chifukwa choti amagwiritsa ntchito luso lawo la kuganiza.*
3 Moyo wosatha adzaupeza+ akamaphunzira ndi kudziwa za inu, Mulungu yekhayo amene ndi woona,+ komanso za Yesu Khristu, amene inu munamutuma.+
14 Koma chakudya chotafuna ndi cha anthu aakulu mwauzimu, amene amatha kusiyanitsa zoyenera ndi zosayenera chifukwa choti amagwiritsa ntchito luso lawo la kuganiza.*