Ezekieli 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Iwe mwana wa munthu, kodi mwambi umene anthu amʼdziko la Isiraeli mukunena wakuti, ‘Masiku akupita koma palibe masomphenya amene akwaniritsidwa,’+ umatanthauza chiyani? Ezekieli 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Iwe mwana wa munthu, anthu a ku Isiraeli akunena kuti, ‘Masomphenya amene ukuona adzachitika kutsogolo ndipo ukulosera zinthu zimene zidzachitike mʼtsogolo kwambiri.’+
22 “Iwe mwana wa munthu, kodi mwambi umene anthu amʼdziko la Isiraeli mukunena wakuti, ‘Masiku akupita koma palibe masomphenya amene akwaniritsidwa,’+ umatanthauza chiyani?
27 “Iwe mwana wa munthu, anthu a ku Isiraeli akunena kuti, ‘Masomphenya amene ukuona adzachitika kutsogolo ndipo ukulosera zinthu zimene zidzachitike mʼtsogolo kwambiri.’+