Yohane 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Wophunzira ameneyu+ ndi amene akuchitira umboni zinthu zimenezi. Iyeyu ndi amenenso analemba zinthu zimenezi ndipo tikudziwa kuti umboni umene akupereka ndi woona. Machitidwe 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Yesu ameneyo Mulungu anamuukitsa, ndipo tonsefe ndife mboni za nkhani imeneyi.+
24 Wophunzira ameneyu+ ndi amene akuchitira umboni zinthu zimenezi. Iyeyu ndi amenenso analemba zinthu zimenezi ndipo tikudziwa kuti umboni umene akupereka ndi woona.