1 Yohane 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Abale okondedwa, musamakhulupirire mawu alionse ouziridwa,*+ koma muzifufuza mawu ouziridwawo* kuti muone ngati alidi ochokera kwa Mulungu,+ chifukwa aneneri abodza* ambiri ayamba kupezeka mʼdzikoli.+
4 Abale okondedwa, musamakhulupirire mawu alionse ouziridwa,*+ koma muzifufuza mawu ouziridwawo* kuti muone ngati alidi ochokera kwa Mulungu,+ chifukwa aneneri abodza* ambiri ayamba kupezeka mʼdzikoli.+