1 Yohane 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana okondedwa, inu ndi ochokera kwa Mulungu, ndipo mwagonjetsa aneneri abodzawo.+ Zili choncho chifukwa amene ali wogwirizana ndi inu+ ndi wamkulu kuposa amene ali wogwirizana ndi dziko.+
4 Ana okondedwa, inu ndi ochokera kwa Mulungu, ndipo mwagonjetsa aneneri abodzawo.+ Zili choncho chifukwa amene ali wogwirizana ndi inu+ ndi wamkulu kuposa amene ali wogwirizana ndi dziko.+