1 Yohane 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mantha amatichititsa kukhala omangika. Koma munthu amene amakonda Mulungu sachita mantha,+ chifukwa chikondi chimene chili chokwanira chimathetsa mantha. Munthu amene amachita mantha, chikondi chake si chokwanira.+
18 Mantha amatichititsa kukhala omangika. Koma munthu amene amakonda Mulungu sachita mantha,+ chifukwa chikondi chimene chili chokwanira chimathetsa mantha. Munthu amene amachita mantha, chikondi chake si chokwanira.+