Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova ali kutali ndi anthu oipa,Koma amamva pemphero la anthu olungama.+