Yohane 13:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mofanana ndi mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana choncho.+ 2 Yohane 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero ndikukupemphani mayi, kuti tizikondana. (Sindikukulemberani lamulo latsopano, koma lomwe lija limene takhala nalo kuyambira pachiyambi.)+
34 Ndikukupatsani lamulo latsopano, kuti muzikondana. Mofanana ndi mmene ine ndakukonderani,+ inunso muzikondana choncho.+
5 Chotero ndikukupemphani mayi, kuti tizikondana. (Sindikukulemberani lamulo latsopano, koma lomwe lija limene takhala nalo kuyambira pachiyambi.)+