Yohane 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Yesu anawauza kuti: “Kuwala kukhalabe pakati panu kanthawi pangʼono. Yendani pamene kuwalako mudakali nako, kuti mdima usakugwereni. Aliyense amene akuyenda mumdima sadziwa kumene akupita.+
35 Yesu anawauza kuti: “Kuwala kukhalabe pakati panu kanthawi pangʼono. Yendani pamene kuwalako mudakali nako, kuti mdima usakugwereni. Aliyense amene akuyenda mumdima sadziwa kumene akupita.+