Aheberi 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho, abale athu oyera, amene muli mʼgulu la anthu oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+
3 Choncho, abale athu oyera, amene muli mʼgulu la anthu oitanidwa kumwamba,+ ganizirani za Yesu, mtumwi ndi mkulu wa ansembe amene tikumuvomereza.+