2 Petulo 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma angelo, ngakhale kuti ndi amphamvu kwambiri, saneneza aphunzitsi abodzawo ndi mawu onyoza, chifukwa angelowo amalemekeza Yehova.*+
11 Koma angelo, ngakhale kuti ndi amphamvu kwambiri, saneneza aphunzitsi abodzawo ndi mawu onyoza, chifukwa angelowo amalemekeza Yehova.*+