Zekariya 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako mngelo wa Yehovayo anauza Satana kuti: “Iwe Satana, Yehova akudzudzule!+ Yehova amene wasankha Yerusalemu+ akudzudzule. Kodi munthu uyu sali ngati chikuni chimene chapulumutsidwa pamoto kuti chisapse?”
2 Kenako mngelo wa Yehovayo anauza Satana kuti: “Iwe Satana, Yehova akudzudzule!+ Yehova amene wasankha Yerusalemu+ akudzudzule. Kodi munthu uyu sali ngati chikuni chimene chapulumutsidwa pamoto kuti chisapse?”