12 Ndipo anthu amenewa, mofanana ndi nyama zopanda nzeru zimene zimangochita zinthu mwachibadwa komanso zimabadwa kuti zidzagwidwe ndi kuwonongedwa, amalankhula monyoza za zinthu zimene sakuzidziwa.+ Anthu amenewa adzawonongedwa chifukwa cha zochita zawo zoipa,