-
2 Petulo 2:15, 16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Asocheretsedwa chifukwa anasiya njira yowongoka. Atsatira njira ya Balamu+ mwana wa Beori, amene anachita zinthu zoipa chifukwa chofunitsitsa kulandira mphoto,+ 16 koma anadzudzulidwa chifukwa cholephera kuchita zinthu zabwino.+ Bulu amene salankhula, analankhula ngati munthu nʼkulepheretsa zochita zamisala za mneneriyo.+
-