Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 33:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Iye anati:

      “Yehova anabwera kuchokera ku Sinai,+

      Anawala pa iwo kuchokera ku Seiri.

      Anawala mwa ulemerero kuchokera kudera lamapiri la Parana,+

      Ndipo anali ndi angelo ake ambirimbiri,*+

      Kudzanja lake lamanja kunali asilikali ake.+

  • Danieli 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mtsinje wa moto unkayenda kuchokera kwa iye.+ Panali atumiki okwana 1 miliyoni* amene ankatumikira nthawi zonse ndi atumiki enanso 100 miliyoni* amene ankatumikira pamaso pake nthawi zonse.+ Bwalo la milandu+ linayamba kuzenga mlandu ndipo mabuku anatsegulidwa.

  • Zekariya 14:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Inu mudzathawira kuchigwa chimene chidzakhale pakati pa mapiri anga, chifukwa chigwacho chidzafika mpaka ku Azeli. Mudzathawa ngati mmene munathawira chivomerezi chimene chinachitika mʼmasiku a Uziya, mfumu ya Yuda.+ Ndipo Yehova Mulungu wanga adzabwera limodzi ndi oyera onse.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena