1 Akorinto 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tisakhalenso ongʼungʼudza, ngati mmene ena a iwo anachitira,+ nʼkuphedwa ndi mngelo wowononga.+ Afilipi 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukamachita zinthu muzipewa kungʼungʼudza+ komanso kukangana+